Ekisodo 34:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Muzichita Chikondwerero cha Masabata,* ndipo pochita chikondwerero chimenechi muzipereka tirigu woyamba kucha pa tirigu amene mwakolola. Kumapeto kwa chaka muzichita Chikondwerero cha Zokolola.*+
22 Muzichita Chikondwerero cha Masabata,* ndipo pochita chikondwerero chimenechi muzipereka tirigu woyamba kucha pa tirigu amene mwakolola. Kumapeto kwa chaka muzichita Chikondwerero cha Zokolola.*+