Ekisodo 34:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mitundu ya anthu ndidzaithamangitsira kutali ndi inu,+ ndipo ndidzakulitsa dera lanu. Palibe aliyense amene adzasirire dziko lanu mukapita kukaona nkhope ya Yehova Mulungu wanu katatu pa chaka. Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:24 Nsanja ya Olonda,9/1/1998, tsa. 20
24 Mitundu ya anthu ndidzaithamangitsira kutali ndi inu,+ ndipo ndidzakulitsa dera lanu. Palibe aliyense amene adzasirire dziko lanu mukapita kukaona nkhope ya Yehova Mulungu wanu katatu pa chaka.