Ekisodo 34:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti ndidzathamangitsira mitunduyo kutali ndi inu,+ ndipo ndidzakuza dera lanu.+ Palibe aliyense adzasirira dziko lanu pamene mwachoka kukaona nkhope ya Yehova Mulungu wanu katatu pa chaka.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 34:24 Nsanja ya Olonda,9/1/1998, tsa. 20
24 Pakuti ndidzathamangitsira mitunduyo kutali ndi inu,+ ndipo ndidzakuza dera lanu.+ Palibe aliyense adzasirira dziko lanu pamene mwachoka kukaona nkhope ya Yehova Mulungu wanu katatu pa chaka.+