-
Ekisodo 38:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kumbali imodzi ya khomo la bwalo, mpanda wa nsaluwo unali mamita 7. Kunali zipilala zitatu ndi zitsulo zitatu zokhazikapo zipilalazo.
-