Ekisodo 38:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kumbali imodzi ya chipata cha bwalo, mpanda wa nsaluwo unali mikono 15. Kunali nsanamira zitatu ndi zitsulo zitatu zokhazikapo nsanamirazo.+
14 Kumbali imodzi ya chipata cha bwalo, mpanda wa nsaluwo unali mikono 15. Kunali nsanamira zitatu ndi zitsulo zitatu zokhazikapo nsanamirazo.+