-
Levitiko 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kenako aziika dzanja lake pamutu pa nkhosayo ndipo iziphedwa patsogolo pa chihema chokumanako. Akatero ana a Aroni aziwaza magazi ake mbali zonse za guwa lansembe.
-