Levitiko 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamenepo aziika dzanja lake pamutu+ pa nkhosayo, ndipo aziipha+ patsogolo pa chihema chokumanako. Akatero, ana a Aroni aziwaza magazi ake mozungulira guwa lansembe.
8 Pamenepo aziika dzanja lake pamutu+ pa nkhosayo, ndipo aziipha+ patsogolo pa chihema chokumanako. Akatero, ana a Aroni aziwaza magazi ake mozungulira guwa lansembe.