Levitiko 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Wansembe wodzozedwa amene adzalowe mʼmalo mwake, kuchokera pakati pa ana ake,+ azipereka nsembeyo. Aziwotcha nsembe yonseyo kuti ikhale nsembe yoperekedwa kwa Yehova. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale.
22 Wansembe wodzozedwa amene adzalowe mʼmalo mwake, kuchokera pakati pa ana ake,+ azipereka nsembeyo. Aziwotcha nsembe yonseyo kuti ikhale nsembe yoperekedwa kwa Yehova. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale.