Levitiko 6:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndipo wansembe, amene adzadzozedwa kulowa m’malo mwake, wochokera pakati pa ana ake,+ azipereka nsembeyo. Azitentha nsembe yonseyo kuti ikhale nsembe+ yoperekedwa kwa Yehova. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale.
22 Ndipo wansembe, amene adzadzozedwa kulowa m’malo mwake, wochokera pakati pa ana ake,+ azipereka nsembeyo. Azitentha nsembe yonseyo kuti ikhale nsembe+ yoperekedwa kwa Yehova. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale.