Levitiko 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Wansembe aziona chotupacho.+ Ngati chikuoneka kuti chayambira mkati mwa khungu ndipo cheya chake chasanduka choyera, wansembe azigamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Imeneyo ndi nthenda ya khate ndipo yatuluka pachithupsacho.
20 Wansembe aziona chotupacho.+ Ngati chikuoneka kuti chayambira mkati mwa khungu ndipo cheya chake chasanduka choyera, wansembe azigamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Imeneyo ndi nthenda ya khate ndipo yatuluka pachithupsacho.