Levitiko 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo wansembe azimuona,+ ndipo ngati chikuoneka kuti n’chozama kupitirira khungu, ndipo cheya chake chasanduka choyera, pamenepo wansembe azigamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Imeneyo ndi nthenda ya khate. Yabuka pachithupsa.
20 Pamenepo wansembe azimuona,+ ndipo ngati chikuoneka kuti n’chozama kupitirira khungu, ndipo cheya chake chasanduka choyera, pamenepo wansembe azigamula kuti munthuyo ndi wodetsedwa. Imeneyo ndi nthenda ya khate. Yabuka pachithupsa.