Levitiko 13:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma ngati nthendayo ikuoneka kuti sinafalikire ndipo pamalopo pamera tsitsi lakuda, ndiye kuti nthendayo yatha. Munthuyo ndi woyera ndipo wansembe azigamula kuti ndi woyera.+
37 Koma ngati nthendayo ikuoneka kuti sinafalikire ndipo pamalopo pamera tsitsi lakuda, ndiye kuti nthendayo yatha. Munthuyo ndi woyera ndipo wansembe azigamula kuti ndi woyera.+