Levitiko 13:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Koma ngati nthenda yothothola tsitsiyo ikuoneka kuti yasiya, ndipo pamera tsitsi lakuda, ndiye kuti nthendayo yatha. Munthuyo ndi woyera, ndipo wansembe azigamula kuti ndi woyera.+
37 Koma ngati nthenda yothothola tsitsiyo ikuoneka kuti yasiya, ndipo pamera tsitsi lakuda, ndiye kuti nthendayo yatha. Munthuyo ndi woyera, ndipo wansembe azigamula kuti ndi woyera.+