Levitiko 13:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Akaona nthendayo pa tsiku la 7 nʼkupeza kuti yafalikira pachovala, mulitali kapena mulifupi, kapena pachikopa (kaya chikopacho amachigwiritsa ntchito yotani), nthendayo ndi khate loopsa ndipo chinthucho nʼchodetsedwa.+
51 Akaona nthendayo pa tsiku la 7 nʼkupeza kuti yafalikira pachovala, mulitali kapena mulifupi, kapena pachikopa (kaya chikopacho amachigwiritsa ntchito yotani), nthendayo ndi khate loopsa ndipo chinthucho nʼchodetsedwa.+