Levitiko 13:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Akaona nthendayo pa tsiku la 7, n’kupeza kuti nthendayo yafalikira pachovala, m’litali kapena m’lifupi,+ kapena pachikopa, kaya amachigwiritsa ntchito yotani, nthendayo ndi khate loopsa.+ Chinthucho ndi chodetsedwa.
51 Akaona nthendayo pa tsiku la 7, n’kupeza kuti nthendayo yafalikira pachovala, m’litali kapena m’lifupi,+ kapena pachikopa, kaya amachigwiritsa ntchito yotani, nthendayo ndi khate loopsa.+ Chinthucho ndi chodetsedwa.