-
Levitiko 14:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Munthu amene akudziyeretsayo azichapa zovala zake ndi kumeta tsitsi lake lonse, kenako azisamba ndipo azikhala woyera. Akatero angathe kulowa mumsasa, koma azikhala kunja kwa tenti yake kwa masiku 7.
-