Levitiko 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ndiyeno wodziyeretsayo azichapa zovala zake+ ndi kumeta tsitsi lake lonse, kenako azisamba+ ndipo azikhala woyera. Akatero, angathe kulowa mumsasa, koma azikhala kunja kwa hema wake masiku 7.+
8 “Ndiyeno wodziyeretsayo azichapa zovala zake+ ndi kumeta tsitsi lake lonse, kenako azisamba+ ndipo azikhala woyera. Akatero, angathe kulowa mumsasa, koma azikhala kunja kwa hema wake masiku 7.+