Levitiko 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Wansembe adzapereke nsembe yamachimo+ nʼkuphimba machimo a munthu amene akudziyeretsayo. Kenako wansembe adzaphe nyama ya nsembe yopsereza.
19 Wansembe adzapereke nsembe yamachimo+ nʼkuphimba machimo a munthu amene akudziyeretsayo. Kenako wansembe adzaphe nyama ya nsembe yopsereza.