Levitiko 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Pamenepo wansembe azipereka nsembe yamachimo+ ndi kuphimba machimo a munthu amene akudziyeretsa ku chodetsa chakeyo. Kenako wansembe azipha nyama ya nsembe yopsereza.
19 “Pamenepo wansembe azipereka nsembe yamachimo+ ndi kuphimba machimo a munthu amene akudziyeretsa ku chodetsa chakeyo. Kenako wansembe azipha nyama ya nsembe yopsereza.