-
Levitiko 14:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Ndiyeno mafuta amene atsala pachikhatho cha wansembe aziwapaka pamutu pa munthu amene akudziyeretsayo, kuti amuphimbire machimo ake pamaso pa Yehova.
-