Levitiko 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno mafuta otsala pachikhatho cha wansembe aziwapaka pamutu+ pa munthu amene akudziyeretsayo, kuti am’phimbire machimo ake pamaso pa Yehova.
29 Ndiyeno mafuta otsala pachikhatho cha wansembe aziwapaka pamutu+ pa munthu amene akudziyeretsayo, kuti am’phimbire machimo ake pamaso pa Yehova.