Levitiko 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 wansembe azituluka mʼnyumbamo nʼkukaima pakhomo, ndipo azitseka nyumbayo masiku 7.+