Levitiko 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 wansembe azituluka m’nyumbamo n’kukaima pakhomo, ndipo azitseka+ nyumbayo masiku 7.