Levitiko 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti moyo wa nyama uli m’magazi+ ndipo ine ndakuikirani magazi paguwa lansembe kuti azikuphimbirani machimo.+ Zili choncho popeza magazi+ ndiwo amaphimba machimo,+ chifukwa moyo uli m’magaziwo. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:11 ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, tsa. 75 Nsanja ya Olonda,6/15/2004, ptsa. 15-166/15/1991, tsa. 9
11 Pakuti moyo wa nyama uli m’magazi+ ndipo ine ndakuikirani magazi paguwa lansembe kuti azikuphimbirani machimo.+ Zili choncho popeza magazi+ ndiwo amaphimba machimo,+ chifukwa moyo uli m’magaziwo.
17:11 ‘Mulungu Apitirize Kukukondani’, tsa. 75 Nsanja ya Olonda,6/15/2004, ptsa. 15-166/15/1991, tsa. 9