Levitiko 24:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno panali mnyamata wina amene mayi wake anali Mwisiraeli, koma bambo wake anali Mwiguputo.+ Mnyamatayu analowa pakati pa ana a Isiraeli ndipo anayamba kulimbana ndi Mwisiraeli+ wina mumsasa.
10 Ndiyeno panali mnyamata wina amene mayi wake anali Mwisiraeli, koma bambo wake anali Mwiguputo.+ Mnyamatayu analowa pakati pa ana a Isiraeli ndipo anayamba kulimbana ndi Mwisiraeli+ wina mumsasa.