-
Levitiko 25:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Kenako mudzadzala mbewu mʼchaka cha 8, ndipo mudzapitiriza kudya chakudya chimene munakolola chija mpaka mʼchaka cha 9. Mudzadya chakalecho mpaka mutakololanso china.
-