-
Levitiko 25:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Mudzalima minda yanu m’chaka cha 8, ndipo mudzakhala mukudyabe chakudya chimene munakolola chija kufikira m’chaka cha 9. Mudzadya chakalecho kufikira mutakololanso china.
-