-
Levitiko 25:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Koma ngati munthu amene anagulitsa malo sanapeze ndalama zoti angabwezere kwa amene anagulayo, malo amene anagulitsawo apitirizebe kukhala a munthu amene anawagulayo mpaka Chaka cha Ufulu chitafika.+ Mʼchaka chimenecho malowo azibwezedwa kwa mwiniwake ndipo amene anagulitsa maloyo azibwerera kumalo akewo.+
-