Levitiko 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chaka cha 50 chizidzakhala chopatulika ndipo muzidzalengeza ufulu kwa anthu onse okhala mʼdzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu kwa inu, ndipo aliyense azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+ Levitiko 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 MʼChaka cha Ufulu chimenechi, aliyense wa inu azibwerera kumalo ake.+
10 Chaka cha 50 chizidzakhala chopatulika ndipo muzidzalengeza ufulu kwa anthu onse okhala mʼdzikolo.+ Chizikhala Chaka cha Ufulu kwa inu, ndipo aliyense azibwerera kumalo ake ndi kubanja lake.+