Levitiko 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Munthu akagulitsa nyumba mumzinda wokhala ndi mpanda, azikhala ndi ufulu woiwombola+ chaka chimodzi chisanathe kuchokera pamene anaigulitsa. Azikhala ndi ufulu umenewu kwa chaka chathunthu.
29 Munthu akagulitsa nyumba mumzinda wokhala ndi mpanda, azikhala ndi ufulu woiwombola+ chaka chimodzi chisanathe kuchokera pamene anaigulitsa. Azikhala ndi ufulu umenewu kwa chaka chathunthu.