Levitiko 25:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘Munthu akagulitsa nyumba mumzinda wokhala ndi linga, azikhala ndi ufulu woiwombola chaka chimodzi chisanathe kuchokera pamene anaigulitsa. Azikhala ndi ufulu umenewu+ kwa chaka chathunthu.
29 “‘Munthu akagulitsa nyumba mumzinda wokhala ndi linga, azikhala ndi ufulu woiwombola chaka chimodzi chisanathe kuchokera pamene anaigulitsa. Azikhala ndi ufulu umenewu+ kwa chaka chathunthu.