-
Levitiko 25:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Koma nyumba zimene zili mʼmidzi yopanda mpanda zizitengedwa monga mbali ya munda wa kunja kwa mzinda. Ufulu woiwombola uzikhalapobe, ndipo mʼChaka cha Ufulu izibwezedwa kwa mwiniwake.
-