Levitiko 25:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma nyumba zimene zili m’midzi yopanda linga zizitengedwa monga mbali ya munda wa kunja kwa mzinda. Ufulu woiwombola+ uzikhalapobe, ndipo m’Chaka cha Ufulu+ izibwezedwa kwa mwiniwake.
31 Koma nyumba zimene zili m’midzi yopanda linga zizitengedwa monga mbali ya munda wa kunja kwa mzinda. Ufulu woiwombola+ uzikhalapobe, ndipo m’Chaka cha Ufulu+ izibwezedwa kwa mwiniwake.