Levitiko 25:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ine ndine Yehova Mulungu wanu amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo,+ kuti ndikupatseni dziko la Kanani. Ndinachita izi kuti ndikusonyezeni kuti ine ndine Mulungu wanu.+
38 Ine ndine Yehova Mulungu wanu amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo,+ kuti ndikupatseni dziko la Kanani. Ndinachita izi kuti ndikusonyezeni kuti ine ndine Mulungu wanu.+