Levitiko 25:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ine ndine Yehova Mulungu wanu amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo, kuti ndikupatseni dziko la Kanani.+ Ndinachita izi kuti ndikusonyezeni kuti ine ndine Mulungu wanu.+
38 Ine ndine Yehova Mulungu wanu amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo, kuti ndikupatseni dziko la Kanani.+ Ndinachita izi kuti ndikusonyezeni kuti ine ndine Mulungu wanu.+