Levitiko 25:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mʼchaka chimenecho iye ndi ana ake* azichoka nʼkubwerera kwa achibale ake. Azibwerera kumalo a makolo ake.+
41 Mʼchaka chimenecho iye ndi ana ake* azichoka nʼkubwerera kwa achibale ake. Azibwerera kumalo a makolo ake.+