Levitiko 25:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 M’chaka chimenecho iye ndi ana ake amasuke ndi kubwerera kwa achibale ake. Abwerere kumalo a makolo ake.+
41 M’chaka chimenecho iye ndi ana ake amasuke ndi kubwerera kwa achibale ake. Abwerere kumalo a makolo ake.+