Levitiko 25:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Komanso muzigula akapolo kuchokera kwa ana a alendo okhala pakati panu.+ Mungagule akapolo kuchokera kwa iwo ndi kwa ana amene alendowo abereka mʼdziko lanu. Amenewa muziwagula kuti akhale akapolo anu.
45 Komanso muzigula akapolo kuchokera kwa ana a alendo okhala pakati panu.+ Mungagule akapolo kuchokera kwa iwo ndi kwa ana amene alendowo abereka mʼdziko lanu. Amenewa muziwagula kuti akhale akapolo anu.