Levitiko 25:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Muzigulanso akapolo kuchokera kwa ana a alendo okhala pakati panu,+ ndi ku mabanja okhala pakati panu, amene ana a alendowo anaberekera m’dziko lanu. Muzigula amenewa kuti akhale akapolo anu.
45 Muzigulanso akapolo kuchokera kwa ana a alendo okhala pakati panu,+ ndi ku mabanja okhala pakati panu, amene ana a alendowo anaberekera m’dziko lanu. Muzigula amenewa kuti akhale akapolo anu.