-
Levitiko 25:52Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
52 Koma ngati kwatsala zaka zochepa kuti Chaka cha Ufulu chifike, aziwerenga yekha zaka zotsalazo, ndipo azipereka ndalama zodziwombolera zogwirizana ndi zaka zotsalazo.
-