Levitiko 25:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Koma ngati kwatsala zaka zochepa kuti Chaka cha Ufulu chifike,+ aziwerenga zaka zotsalazo, ndipo azipereka ndalama zodziwombolera zogwirizana ndi zaka zotsalazo.
52 Koma ngati kwatsala zaka zochepa kuti Chaka cha Ufulu chifike,+ aziwerenga zaka zotsalazo, ndipo azipereka ndalama zodziwombolera zogwirizana ndi zaka zotsalazo.