Levitiko 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Munthu akapereka nyumba yake kwa Yehova kuti ikhale yopatulika, wansembe aziiona nʼkunena mtengo wake. Mtengowo uzidalira mmene nyumbayo ilili, kaya ndi yabwino kapena ayi. Mtengo umene wansembe wanena uzikhala womwewo.+
14 Munthu akapereka nyumba yake kwa Yehova kuti ikhale yopatulika, wansembe aziiona nʼkunena mtengo wake. Mtengowo uzidalira mmene nyumbayo ilili, kaya ndi yabwino kapena ayi. Mtengo umene wansembe wanena uzikhala womwewo.+