Levitiko 27:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “‘Munthu akapereka* nyumba yake kwa Yehova kuti ikhale yopatulika, wansembe aziiona ndi kunena mtengo wake. Mtengowo uzidalira mmene nyumbayo ilili, kaya ndi yabwino kapena ayi.+ Mtengo umene wansembe wanena uzikhala womwewo.
14 “‘Munthu akapereka* nyumba yake kwa Yehova kuti ikhale yopatulika, wansembe aziiona ndi kunena mtengo wake. Mtengowo uzidalira mmene nyumbayo ilili, kaya ndi yabwino kapena ayi.+ Mtengo umene wansembe wanena uzikhala womwewo.