Levitiko 27:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Asaifufuze ngati ili yabwino kapena yoipa, ndiponso asaisinthanitse ndi ina. Koma ngati waisinthanitsa ndi nyama ina, zonse ziwiri, yoyambayo ndi imene waisinthanitsayo, zizikhala zopatulika.+ Sangathe kuiwombola.’”
33 Asaifufuze ngati ili yabwino kapena yoipa, ndiponso asaisinthanitse ndi ina. Koma ngati waisinthanitsa ndi nyama ina, zonse ziwiri, yoyambayo ndi imene waisinthanitsayo, zizikhala zopatulika.+ Sangathe kuiwombola.’”