Numeri 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo anasonkhanitsa anthu onse pa tsiku loyamba la mwezi wachiwiri kuti munthu aliyense amulembe mʼkaundula mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawalemba mayina kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo+
18 Iwo anasonkhanitsa anthu onse pa tsiku loyamba la mwezi wachiwiri kuti munthu aliyense amulembe mʼkaundula mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawalemba mayina kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo+