Numeri 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mbadwa za Zebuloni,+ anazilemba mayina mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawerenga amuna onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo.
30 Mbadwa za Zebuloni,+ anazilemba mayina mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawerenga amuna onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo.