Numeri 1:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mbadwa za Yosefe za fuko la Efuraimu+ anazilemba mayina mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawerenga amuna onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo.
32 Mbadwa za Yosefe za fuko la Efuraimu+ anazilemba mayina mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawerenga amuna onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo.