Numeri 1:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mbadwa za Manase+ anazilemba mayina mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawerenga amuna onse azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo.
34 Mbadwa za Manase+ anazilemba mayina mogwirizana ndi mabanja awo ndiponso nyumba za makolo awo. Anawerenga amuna onse azaka 20 kupita mʼtsogolo, amene anali oyenera kupita kunkhondo.