Numeri 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Asilikali onse a gulu la Dani amene analembedwa mayina alipo 157,600. Amenewa azikhala omalizira kunyamuka,+ mogwirizana ndi magulu a Aisiraeli a mafuko atatuatatu.”
31 Asilikali onse a gulu la Dani amene analembedwa mayina alipo 157,600. Amenewa azikhala omalizira kunyamuka,+ mogwirizana ndi magulu a Aisiraeli a mafuko atatuatatu.”