Numeri 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Asilikali onse olembedwa mayina a msasa wa Dani alipo 157,600. Amenewa azikhala omalizira kunyamuka,+ malinga ndi zigawo za Aisiraeli za mafuko atatuatatu.”
31 “Asilikali onse olembedwa mayina a msasa wa Dani alipo 157,600. Amenewa azikhala omalizira kunyamuka,+ malinga ndi zigawo za Aisiraeli za mafuko atatuatatu.”